1 Chronicles 22:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Davide adalamulanso atsogoleri onse a ku Israele kuti azithandizana ndi Solomoni mwana wake, adati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Davide analangizanso akalonga a Israele athandize Solomoni mwana wake, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Davide analamula atsogoleri onse a Israeli kuti athandize Solomoni mwana wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Davide analangizanso akalonga a Israyeli athanelize Solomo mwana wace, ndi kuti,