1 Chronicles 22:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Pajatu Chauta Mulungu wanu ali nanu, ndipo adakupatsani mtendere ku mbali zonse. Iye wapereka kwa ine nzika zonse zam'dzikomu, mwakuti zagonjera Chauta ndi inu anthu ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi Yehova Mulungu wanu sali nanu? Sanakupumulitseni pambali ponse? Pakuti anapereka nzika za m'dziko m'dzanja mwanga, ndi dziko lagonjetsedwa pamaso pa Yehova, ndi pamaso pa anthu ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anawawuza kuti, “Kodi Yehova Mulungu, sali nanu? Ndipo Iye siwakupatsani mpumulo mbali zonse? Pakuti Iyeyo wapereka eni nthaka kwa inu ndipo dziko lili pa ulamuliro wa Yehova ndi anthu ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi Yehova Mulungu wanu sali nanu? sanakupumulitsani pambali ponse? pakuti anapereka nzika za m'dziko m'dzanja mwanga, ndi dziko lagonjetsedwa pamaso pa Yehova, ndi pamaso pa anthu ace.