1 Chronicles 22:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaperekanso matabwa osaŵerengeka a mtengo wa mkungudza, chifukwa anthu a ku Sidoni ndi a ku Tiro adaabwera ndi mikungudza yambiri kwa Davide.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi mitengo yamikungudza yosaiwerenga; pakuti Asidoni ndi Atiro anabwera nayo kwa Davide mitengo yamikungudza yochuluka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anaperekanso mitengo yambiri ya mkungudza, yosawerengeka, pakuti anthu a ku Sidoni ndi a ku Turo anabweretsa yambiri kwa Davide.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi mitengo yamikungudza yosaiwerenga; pakuti Asidoni ndi Aturo anabwera nayo kwa Davide mitengo yamikungudza yocuruka,