1 Chronicles 22:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adaitana Solomoni mwana wake, ndipo adamlamula kuti amangire nyumba Chauta, Mulungu wa Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo iye anaitana Solomoni mwana wake, namlangiza ammangire Yehova Mulungu wa Israele nyumba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono iye anayitana Solomoni mwana wake ndipo anamulamula kuti adzamangire nyumba Yehova Mulungu wa Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo iye anaitana Solomo mwana wace, namlangiza ammangire Yehova Mulungu wa Israyeli nyumba.