1 Chronicles 22:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Davide adauza Solomoni kuti, “Mwana wanga, ine ndinkaganiza zakuti ndimangire nyumba Chauta, Mulungu wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Davide anati kwa Solomoni mwana wake, Kunena za ine, kumtima kwanga kudati, ndilimangire dzina la Yehova Mulungu wanga nyumba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide anati kwa Solomoni, “Mwana wanga, ine ndinali ndi maganizo oti ndimangire nyumba Dzina la Yehova Mulungu wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Davide anati kwa Solomo mwana wace, Kunena za ine, kumtima kwanga kudati, ndilimangire dzina la Yehova Mulungu wanga nyumba.