1 Chronicles 23:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Davide atakalamba, masiku ake atatha, adaika Solomoni mwana wake kuti akhale mfumu ya Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atakalamba tsono Davide ndi kuchuluka masiku, iye analonga mwana wake Solomoni akhale mfumu ya Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide atakalamba, ali ndi zaka zambiri, anayika Solomoni mwana wake kukhala mfumu ya Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atakalamba tsono Davide ndi kucuruka masiku, iye analonga mwana wace Solomo akhale mfumu ya Israyeli.