1 Chronicles 23:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ana a Mose, munthu wa Mulungu uja, adaŵawerengera pamodzi ndi fuko la Levi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kunena za Mose munthu wa Mulunguyo, ana ake anatchulidwa mwa fuko la Levi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Mose munthu wa Mulungu anawerengedwa ngati gawo la fuko la Levi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kunena za Mose munthu wa Mulunguyo, ana ace anaehulidwa mwa pfuko la Levi.