1 Chronicles 23:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Eleazara adafa opanda ana aamuna, koma aakazi okhaokha. Abale ao, ana a Kisi, ndiwo amene adaŵakwatira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nafa Eleazara wopanda ana amuna, koma ana akazi ndiwo; ndi asuweni ao ana a Kisi anawatenga akhale akazi ai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Eliezara anamwalira wopanda ana aamuna. Iye anali ndi ana aakazi okhaokha. Abale awo, ana a Kisi, ndiwo amene anawakwatira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nafa Eleazara wopanda ana amuna, koma ana akazi ndiwo; ndi asuweni ao ana a Kisi anawatenga akhale akazi ao.