1 Chronicles 23:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Potsata mau omalizira a Davidewo, ameneŵa ndiwo anali chiŵerengero cha Alevi, kuyambira anthu a zaka makumi aŵiri ndi kupitirirapo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti monga mwa mau ake otsiriza a Davide, ana a Levi anawerengedwa kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Potsata malangizo otsiriza a Davide, Alevi anawerengedwa kuyambira amuna a zaka makumi awiri zakubadwa kapena kupitirirapo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti monga mwa mau ace otsiriza a Davide, ana a Levi anawerengedwa kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu.