1 Chronicles 23:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adati, “Mwa ameneŵa anthu 24,000 adzakhale oyang'anira ntchito za m'Nyumba ya Chauta. Anthu 6,000 adzakhale nduna ndi aweruzi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
A iwowa zikwi makumi awiri mphambu zinai anayang'anira ntchito ya nyumba ya Yehova, ndi zikwi zisanu ndi chimodzi ndiwo akapitao ndi oweruza,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide anati, “Mwa amenewa, amuna 24,000 aziyangʼanira ntchito za mʼNyumba ya Mulungu ndipo 6,000 akhale akuluakulu ndi oweruza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
A iwowa zikwi makumi awiri mphambu zinai anayang'anira nchito ya nyumba ya Yehova, ndi zikwi zisanu ndi cimodzi ndiwo akapitao ndi oweruza,