1 Chronicles 24:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atsogoleri ena a mabanja a Levi naŵa: Yedeiya, mdzukulu wa Subaele, amene anali mdzukulu wa Amuramu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo wa ana otsala a Levi: wa ana a Amuramu, Subaele; wa ana a Subaele, Yedeiya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Za zidzukulu zina zonse za Levi: Kuchokera kwa ana a Amramu: Subaeli; kuchokera kwa ana a Subaeli: Yehideya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo wa ana otsala a Levi: wa ana a Amiramu, Subaeli; wa ana a Subaeli, Yedeya.