1 Chronicles 24:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
achisanu adagwera Malikiya, achisanu ndi chimodzi adagwera Miyamini,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
wachisanu Malikiya, wachisanu ndi chimodzi Miyamini,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
achisanu anagwera Malikiya, achisanu ndi chimodzi anagwera Miyamini,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
wacisanu Malikiya, wacisanu ndi cimodzi Miyamini,