1 Chronicles 25:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onseŵa anali ana a Hemani, mneneri wa mfumu, potsata malonjezo a Mulungu akuti adzamkweza iyeyo. Pakuti Mulungu adaampatsa Hemaniyo ana aamuna 14 ndi ana aakazi atatu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
awa onse ndiwo ana a Hemani mlauli wa mfumu m'mau a Mulungu, kuti akweze mphamvu yake. Ndipo Mulungu anapatsa Hemani ana amuna khumi ndi anai, ndi ana akazi atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onsewa anali ana a Hemani mlosi wa mfumu. Iye anapatsidwa anawa potsata mawu a Mulungu akuti adzamukweza. Mulungu anapatsa Hemani ana aamuna 14 ndi ana aakazi atatu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
awa onse ndiwo ana a Hemani mlauli wa mfumu m'mau a Mulungu, kuti akweze mphamvu yace. Ndipo Mulungu anapatsa Hemani ana amuna khumi ndi anai, ndi ana akazi atatu.