1 Chronicles 26:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Magulu a alonda odikira pa khomo naŵa: m'gulu la Akora munali Meselemiya, mwana wa Kore, mmodzi mwa ana a Asafu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
A magawidwe a odikira a Akora: Meselemiya mwana wa Kore wa ana a Asafu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Magulu a alonda a pa zipata: Kuchokera ku banja la Kora: Meselemiya mwana wa Kore, mmodzi mwa ana a Asafu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
A magawidwe a odikira a Akora: Meselemiya mwana wa Kore wa ana a Asafu.