1 Chronicles 26:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wachiŵiri Hilikiya, wachitatu Tebaliya, wachinai anali Zekariya. Onse a m'banja la Hosa amene anali alonda analipo 13.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
wachiwiri Hilikiya, wachitatu Tebaliya, wachinai Zekariya; ana ndi abale onse a Hosa ndiwo khumi ndi atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
wachiwiri Hilikiya, wachitatu Tebaliya ndipo wachinayi Zekariya. Ana ndi abale onse a Hosa analipo 13.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
waciwiri Hilikiya, wacitatu Tebaliya, wacinai Zekariya; ana ndi abale onse a Hosa ndiwo khumi ndi atatu.