1 Chronicles 26:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwonso adachita maere pa mabanja onse ang'onoang'ono ndi akuluakulu omwe, kuti apeze okalonda pa makomo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anachita maere ang'ono ndi akulu, monga mwa nyumba za makolo ao, kuchitira zipata zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anachita maere mwa mabanja awo aangʼono ndi aakulu omwe kuti apeze mlonda pa chipata chilichonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anacita maere ang'ono ndi akuru, monga mwa nyumba za makolo ao, kucitira zipata zonse.