1 Chronicles 26:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Selemiya adamsankha kuti azilonda pa khomo lakuvuma. Mwana wake Zekariya, phungu wanzeru, adamsankha kuti azilonda khomo lakumpoto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi maere a kum'mawa anagwera Selemiya. Ndipo anachitira maere Zekariya mwana wake, phungu wanzeru, ndi maere anamgwera kumpoto;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Maere a chipata chakummwa anagwera Selemiya. Maere anachitikanso chifukwa cha mwana wake Zekariya, phungu wanzeru ndipo maere a chipata chakumpoto anagwera iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi maere a kum'mawa anagwera Selemiya. Ndipo anacitira maere Zekariya mwana wace, phungu wanzeru, ndi maere anamgwera kumpoto;