1 Chronicles 26:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuvuma kunkakhala alonda asanu ndi mmodzi tsiku lililonse. Kumpoto kunkakhala alonda anai tsiku lililonse, kumwera alonda anai tsiku lililonse, ndiponso alonda aŵiriaŵiri ku nyumba ya katundu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kum'mawa kunali Alevi asanu ndi mmodzi, kumpoto anai tsiku ndi tsiku, kumwera anai tsiku ndi tsiku, ndi a nyumba ya akatundu awiri ndi awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mbali ya kummawa kunkakhala Alevi 6 pa tsiku, kumpoto anayi pa tsiku, kummwera anayi pa tsiku ndipo awiri ankakhala pa nyumba yosungiramo katundu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kum'mawa kunali Alevi asanu ndi mmodzi, kumpoto anai tsiku ndi tsiku, kumwela anai tsiku ndi tsiku, ndi a nyumba ya akatundu awiri ndi awiri.