1 Chronicles 26:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Meselemiya anali ndi ana aŵa: wachisamba anali Zekariya, wachiŵiri Yediyale, wachitatu Zebadiya, wachinai Yatiniele,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Meselemiya anali ndi ana, woyamba Zekariya, wachiwiri Yediyaele, wachitatu Zebadiya, wachinai Yatiniele,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Meselemiya anali ndi ana awa: woyamba Zekariya, wachiwiri Yediaeli, wachitatu Zebadiya, wachinayi Yatinieli,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Meselemiya anali ndi ana, woyamba Zekariya, waciwiri Yedyaeli, wacitatu Zebadiya, wacinai Yatiniyeli,