1 Chronicles 26:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwa Alevi, Ahiya ankayang'anira chuma cha ku Nyumba ya Chauta ndiponso zipinda zosungiramo zinthu zopatsidwa kwa Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo wa Alevi, Ahiya anayang'anira chuma cha nyumba ya Mulungu, ndi chuma cha zopatulika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abale awo Alevi, motsogozedwa ndi Ahiya, anali oyangʼanira chuma cha nyumba ya Mulungu ndi zinthu zoperekedwa kwa Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo wa Alevi, Ahiya anayang'anira cuma ca nyumba ya Mulungu, ndi cuma ca zopatulika.