1 Chronicles 26:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ladani, mmodzi mwa ana a Geresoni, adabereka ana ake amene ankakhala atsogoleri a mabanja, makamaka Ayehiyeli.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Ladani: ana a Ladani a Ageresoni, akulu a nyumba za makolo a Ladani Mgeresoni, Yehiyeli.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adzukulu a Ladani, mmodzi mwa ana a Geresoni, amene anali atsogoleri a mabanja a Ageresoni, anali awa: Yehieli,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Ladani: ana a Ladani a Agerisoni, akuru a nyumba za makolo a Ladani Mgerisoni, Yehieli.