1 Chronicles 26:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana ena a Ladani, Zetamu ndi Yowele mbale wake, nawonso ankayang'anira chuma cha ku Nyumba ya Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Yehiyeli: Zetamu ndi Yowele mbale wake, oyang'anira chuma cha nyumba ya Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ana a Yehieli, Zetamu ndi mʼbale wake Yoweli. Iwo amayangʼanira chuma cha ku Nyumba ya Mulungu wa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Yehieli: Zetamu ndi Yoeli mbale wace, oyang'anira cuma ca nyumba ya Yehova.