1 Chronicles 26:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Abale ake obadwa mwa Eliyezere anali Rehabiya mwana wake, Yesaiya, Yoramu, Zakiri ndiponso Selomoti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi abale ake a Eliyezere: Rehabiya mwana wake, ndi Yesaya mwana wake ndi Yoramu mwana wake, ndi Zikiri mwana wake, ndi Selomoti mwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abale ake obadwa mwa Eliezara, anali Rekabiya mwana wake, Yesaya mwana wake, Yoramu mwana wake, Zikiri mwana wake ndi Selomiti mwana wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi abale ace a Eliezeri: Rehabiya mwana wace, ndi Yesava mwana wace ndi Yorramu mwana wace, ndi Zikiri mwana wace, ndi Selomoti mwana wace.