1 Chronicles 26:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwa zidzukulu za Izara, Kenaniya ndi ana ake ndiwo adaŵaika kuti azigwirira Aisraele ntchito zoyang'anira zinthu, monga zolembalemba ndiponso kuweruza milandu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
A Aizihara: Kenaniya ndi ana ake anachita ntchito ya pabwalo ya Israele, akapitao ndi oweruza milandu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuchokera ku banja la Izihari: Kenaniya ndi ana ake anapatsidwa ntchito kutali ndi Nyumba ya Mulungu ngati akuluakulu ndi oweruza Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
A Aizara: Kenaniya ndi ana ace anacita nchito ya pabwalo ya Israyeli, akapitao ndi oweruza mirandu.