1 Chronicles 26:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Obededomu Mulungu anali ndi ana aŵa: wachisamba anali Semaya, wachiŵiri Yehozabadi, wachitatu Yowa, wachinai Sakara, wachisanu Netanele,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Obededomu anali nao ana, woyamba Semaya, wachiwiri Yehozabadi, wachitatu Yowa, wachinai Sakara, wachisanu Netanele,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Obedi-Edomu analinso ndi ana awa: woyamba Semaya, wachiwiri Yehozabadi, wachitatu Yowa, wachinayi Sakara, wachisanu Netaneli,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Obedi Edomu anali nao ana, woyamba Semaya, waciwiri Yozabadi, wacitatu Yowa, wacinai Sakara, wacisanu Netaneli,