1 Chronicles 26:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Semaya mwana wake nayenso anali ndi ana amene anali otchuka m'mabanja a makolo ao, makamaka aŵiri omariza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Semaya mwana wake yemwe kunabadwa ana, akulamulira nyumba ya atate wao; pakuti anali ngwazi zamphamvu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wake Semaya analinso ndi ana amene anali atsogoleri mʼbanja la abambo awo chifukwa anali anthu amphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kwa Semaya mwana wace yemwe kunabadwa ana, akulamulira nyumba ya atate wao; pakuti anali ngwazi zamphamvu.