1 Chronicles 27:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtsogoleri pa mwezi wachisanu ndi chitatu anali Sibekai Muhusa, wa m'banja la Zera. Pa gulu lake panali asilikali 24,000.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wachisanu ndi chitatu wa mwezi wachisanu ndi chitatu ndiye Sibekai Muhusa wa Azera; ndi m'chigawo mwake zikwi makumi awiri mphambu zinai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wa 8 pa mwezi wa 8 anali Sibekai Mhusati, wa mbumba ya Zera. Pa gulu lake panali asilikali 24,000
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wacisanu ndi citatu wa mwezi wacisanu ndi citatu ndiye Sibekai Mhusati wa Afera; ndi m'cigawo mwace zikwi makumi awiri mphambu zinai.