1 Chronicles 27:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtsogoleri pa mwezi wachikhumi anali Maharai, wa ku Netofa, wa m'banja la Zera. Pa gulu lake panali asilikali 24,000.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wakhumi wa mwezi wakhumi ndiye Maharai Mnetofa wa Azera; ndi m'chigawo mwake zikwi makumi awiri mphambu zinai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wa khumi pa mwezi wa khumi anali Mahazayi wa ku Netofa, wa mbumba ya Zera. Pa gulu lake panali asilikali 24,000.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wakhumi wa mwezi wakhumi ndiye Maharai Mnetofati wa Azera; ndi m'cigawo mwace zikwi makumi awiri mphambu zinai.