1 Chronicles 27:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atsogoleri amene ankayang'anira mafuko a Aisraele anali aŵa: Mtsogoleri wa Arubeni anali Eliyezere, mwana wa Zikiri. Mtsogoleri wa Asimeoni anali Sefatiya, mwana wa Maaka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma oyang'anira mafuko a Israele ndi awa: wa Arubeni mtsogoleri wao ndiye Eliyezere mwana wa Zikiri; wa Asimeoni, Sefatiya mwana wa Maaka;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akuluakulu amene amatsogolera mafuko a Israeli ndi awa: Mtsogoleri wa fuko la Rubeni: Eliezara mwana wa Zikiri; mtsogoleri wa fuko la Simeoni: Sefatiya mwana wa Maaka;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma oyang'anira mafuko a lsrayeli ndi awa: wa Arubeni mtsogoleri wao ndiye Eliezeri mwana wa Zikiri; wa Asimeoni, Sefatiya mwana wa Maaka;