1 Chronicles 27:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtsogoleri wa Ayuda anali Elihu, mmodzi mwa abale a Davide. Mtsogoleri wa Aisakara anali Omuri, mwana wa Mikaele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
wa Yuda, Elihu mbale wina wa Davide; wa Isakara, Omuri mwana wa Mikaele;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mtsogoleri wa fuko la Yuda: Elihu, mʼbale wake wa Davide; mtsogoleri wa fuko la Isakara: Omuri mwana wa Mikayeli;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
wa Yuda, Elihu mbale wina wa Davide; wa Isakara, Omri mwana wa Mikaeli;