1 Chronicles 27:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtsogoleri wa Azebuloni anali Isimaya, mwana wa Obadiya. Mtsogoleri wa Anafutali anali Yeremoti, mwana wa Aziriele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
wa Zebuloni, Isimaya mwana wa Obadiya; wa Nafutali, Yerimoti mwana wa Aziriele;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mtsogoleri wa fuko la Zebuloni: Isimaiya mwana wa Obadiya; mtsogoleri wa fuko la Nafutali: Yerimoti mwana wa Azirieli;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
wa Zebuluni, Isimaya mwana wa Obadiya; wa Nafitali, Yeremoti mwana wa Azrieli;