1 Chronicles 27:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtsogoleri wa Aefuremu anali Hoseya, mwana wa Azaziya. Mtsogoleri wa fuko lahafu la Manase lakuzambwe anali Yowele, mwana wa Pedaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
wa ana a Efuremu, Hoseya mwana wa Azaziya; wa fuko la Manase logawika pakati, Yowele mwana wa Pedaya;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mtsogoleri wa fuko la Efereimu: Hoseya mwana wa Azaziya; mtsogoleri wa fuko la theka la Manase: Yoweli mwana wa Pedaya;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
wa ana a Efraimu, Hoseya mwana wa Azaziya; wa pfuko la Manase logawika pakati, Yoeli mwana wa Pedaya;