1 Chronicles 27:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtsogoleri wa fuko lahafu la Manase lakuvuma, dera la Giliyadi anali Ido, mwana wa Zekariya. Mtsogoleri wa Abenjamini anali Yasiyele, mwana wa Abinere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
wa fuko la Manase logawika pakati m'Giliyadi, Ido mwana wa Zekariya; wa Benjamini, Yaasiyele mwana wa Abinere;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mtsogoleri wa fuko la theka la Manase limene linali ku Giliyadi: Ido mwana wa Zekariya; mtsogoleri wa fuko la Benjamini: Yaasieli mwana wa Abineri;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
wa pfuko la Manase logawika pakati m'Gileadi, Ido mwana wa Zekariya; wa Benjamini, Yasiyeli mwana wa Abineri;