1 Chronicles 27:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Eziri mwana wa Kelubi ankayang'anira anthu ogwira ntchito zolima ku minda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi woyang'anira iwo akugwira ntchito ya m'munda yakulima nthaka ndiye Eziri mwana wa Kelubu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Eziri mwana wa Kelubi ankayangʼanira anthu ogwira ntchito yolima ku munda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi woyang'anira iwo akugwira nchito ya m'munda yakulima nthaka ndiye Ezri mwana wa Kelubi;