1 Chronicles 27:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Baala-Hanani wa ku Gederi anali woyang'anira mitengo ya olivi ndi ya mikuyu ku Sefera. Yowasi ankayang'anira mosungira mafuta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi woyang'anira mitengo ya azitona, ndi yamikuyu yokhala kuzidikha kunsi, ndiye Baala-Hanani Mgederi; ndi woyang'anira zosungiramo mafuta ndiye Yowasi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Baala-Hanani wa ku Gederi ankayangʼanira mitengo ya olivi ndi ya mikuyu ya ku Sefela. Yowasi ankayangʼanira mafuta a Olivi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi woyang'anira mitengo yaazitona, ndi yamikuyu yokhala kuzidikha kunsi, ndiye Baala Hanani Mgederi; ndi woyang'anira zosungiramo mafuta ndiye Yoasi;