1 Chronicles 27:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sitirai wa ku Saroni ankayang'anira ziŵeto za ku busa la ku Saroni. Safati, mwana wa Adilai, ankayang'anira ziŵeto zakuzigwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi woyang'anira ng'ombe zakudya m'Saroni ndiye Sitirai Msaroni; ndi woyang'anira ng'ombe za m'zigwa ndiye Safati mwana wa Adilai;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sitirayi wa ku Saroni ankayangʼanira ziweto zimene amaweta ku Saroni. Safati mwana wa Adilayi ankayangʼanira ngʼombe zakuzigwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi woyang'anira ng'ombe zakudya m'Saroni ndiye Sitirai Msaroni; ndi woyang'anira ng'ombe za m'zigwa ndiye Safabi mwana wa Adilai;