1 Chronicles 27:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ahitofele anali phungu wa mfumu, ndipo Husai Mwariki anali bwenzi la mfumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Ahitofele anali phungu wa mfumu, ndi Husai Mwariki anali bwenzi la mfumu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ahitofele anali phungu wa mfumu. Husai Mwariki anali bwenzi la mfumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Ahitofeli anali phungu wa mfumu, ndi Husai M-ariki anali bwenzi la mfumu;