1 Chronicles 27:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Benaya ameneyu ndiye amene ankatsogolera anthu makumi atatu aja. Amizabadi mwana wake ndiye amene ankatsatana naye polamulira gulu lakelo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Benaya ameneyo ndiye wamphamvu uja wa makumi atatu aja, woyang'anira chigawo chake ndi Amizabadi mwana wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uyu ndi Benaya uja amene anali wamphamvu pa gulu la anthu makumi atatu ndipo ndiye amatsogolera anthu makumi atatu aja. Mwana wake Amizabadi ndiye amatsogolera gulu lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Benaya ameneyo ndiye wamphamvu uja wa makumi atatu aja, woyang'anira makumi atatu aja; woyang'anira cigawo cace ndi Amizabadi mwana wace.