1 Chronicles 27:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Asahele, mbale wake wa Yowabu, anali mtsogoleri pa mwezi wachinai, ndipo mwana wake Zebadiya adaloŵa m'malo mwake. Pa gulu lake panali asilikali 24,000.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wachinai wa mwezi wachinai ndiye Asahele mbale wa Yowabu, ndi pambuyo pake Zebadiya mwana wake; ndi m'chigawo mwake munali zikwi makumi awiri mphambu zinai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wachinayi pa mwezi wachinayi anali Asaheli mʼbale wake wa Yowabu; ndipo mwana wake Zebadiya ndiye analowa mʼmalo mwake. Pa gulu lake panali asilikali 24,000.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wacinai wa mwezi wacinai ndiye Asebeli mbale wa Yoabu, ndi pambuyo pace Zebadiya mwana wace; ndi m'cigawo mwace munali zikwi makumi awiri mphambu zinai.