1 Chronicles 27:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtsogoleri pa mwezi wachisanu anali Samuti mdzukulu wa Izara. Pa gulu lake panali asilikali 24,000.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kazembe wachisanu wa mwezi wachisanu ndiye Samuti Mwizara; ndi m'chigawo mwake zikwi makumi awiri mphambu zinai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wachisanu pa mwezi wachisanu anali Samihuti, mdzukulu wa Izira. Pa gulu lake panali asilikali 24,000.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kazembe wacisanu wa mwezi wacisanu ndiye Samuti M-izra; ndi m'cigawo mwace zikwi makumi awiri mphambu zinai.