1 Chronicles 28:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adalangizanso za kulemera kwa golide wopangira ziŵiya zonse zagolide zofunika, kulemera kwa siliva wopangira ziŵiya zasiliva zonse zofunika,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
cha golide woyesedwa kulemera kwake wa zipangizo zagolide, wa zipangizo zonse za ntchito ya mtundu uliwonse; cha siliva wa zipangizo zasiliva woyesedwa kulemera kwake, wa zipangizo za ntchito ya mitundumitundu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anakonzeratu za kulemera kwa golide wopangira zida zonse zagolide zogwirira ntchito zosiyanasiyana, ndiponso kulemera kwa siliva wopangira zida zonse zasiliva zogwirira ntchito zosiyanasiyana:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ca golidi woyesedwa kulemera kwace wa zipangizo zagolidi, wa zipangizo zonse za nchito ya mtundu uli wonse; ca siliva wa zipangizo zasiliva woyesedwa kulemera kwace, wa zipangizo za nchito ya mitundu mitundu;