1 Chronicles 28:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Davide adati, “Zonse ndalembazi zikugwirizana ndi mau amene adalembedwa potsata malangizo a Chauta mwiniwake, ndipo ndidamvetsa bwino kuti ntchito yonseyo iyenera kuchitika potsata mapulaniwo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chonsechi, anati Davide, anandidziwitsa ndi kuchilemba kuchokera kwa dzanja la Yehova; ndizo ntchito zonse za chifaniziro ichi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Davide anati, “Zonsezi ndalemba kuchokera kwa Yehova, ndipo Iye wachita kuti ndimvetsetse zonse za mapulaniwa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Conseci, anati Davide, anandidziwitsa ndi kucilemba kucokera kwa dzanja la Yehova; ndizo nchito zonse za cifaniziro ici.