1 Chronicles 28:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho mwa ana anga onse, potitu Chauta adandipatsa ana ambiri, Iyeyo wasankha Solomoni, kuti akhale pa mpando waufumu wa Chauta ndi kumalamulira Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi mwa ana anga onse (pakuti Yehova wandipatsa ana amuna ambiri), anasankha Solomoni mwana wanga akhale pa mpando wachifumu wa ufumu wa Yehova kuweruza Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa ana anga ambiri onse amene Yehova wandipatsa, Iye wasankha mwana wanga Solomoni kuti akhale pa mpando waufumu wa ufumu wa Yehova kuti alamulire Israeli.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi mwa ana anga onse (pakuti Yehova wandipatsa ana amuna ambiri), anasankha Solomo mwana wanga akhale pa mpando wacifumu wa ufumu wa Yehova kuweruza Israyeli.