1 Chronicles 3:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Naŵa ana a Davide amene adabadwira ku Hebroni. Amoni ndiye mwana wake wachisamba, mai wake anali Ahinowamu, wa ku Yezireele. Daniele ndiye mwana wake wachiŵiri, mai wake anali Abigaile, wa ku Karimele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Davide tsono ombadwira ku Hebroni: woyamba Aminoni wa Ahinowamu wa ku Yezireele, wachiwiri Daniele wa Abigaile wa ku Karimele,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana aamuna a Davide amene anabadwira ku Hebroni anali awa: Woyamba anali Amnoni, amayi ake anali Ahinoamu wa ku Yezireeli; wachiwiri anali Danieli, amayi ake anali Abigayeli wa ku Karimeli;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana Davide tsono ombadwira ku Hebroni: woyamba a Amnoni wa Ahinoamu wa ku Yezreeli, waciwiri Danieli wa Abigaili wa ku Karimeli,