1 Chronicles 3:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nazi zidzukulu za Solomoni: Rehobowamu adabereka Abiya, Abiya adabereka Asa, Asa adabereka Yehosafati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mwana wa Solomoni ndiye Rehobowamu, Abiya mwana wake, Asa mwana wake, Yehosafati mwana wake,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wa Solomoni anali Rehabiamu, Rehabiamu anabereka Abiya, Abiya anabereka Asa, Asa anabereka Yehosafati,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mwana wa Solomo ndiye Rehabiamu, Abiya mwana wace, Asa mwana wace, Yeo hosafati mwana wace,