1 Chronicles 3:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yehosafati adabereka Yoramu. Yoramu adabereka Ahaziya, Ahaziya adabereka Yowasi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yoramu mwana wake, Ahaziya mwana wake, Yowasi mwana wake,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehosafati anabereka Yehoramu, Yehoramu anabereka Ahaziya, Ahaziya anabereka Yowasi,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yoramu mwana wace, Ahaziya mwana wace, Yoasi mwana wace,