1 Chronicles 3:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yowasi adabereka Amaziya, Amaziya adabereka Azariya, Azariya adabereka Yotamu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amaziya mwana wake, Azariya mwana wake, Yotamu mwana wake,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yowasi anabereka Amaziya, Amaziya anabereka Azariya, Azariya anabereka Yotamu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amaziya mwana wace, Azariya mwana wace, Yotamu mwana wace,