1 Chronicles 3:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Yosiya naŵa: Yohanani, mwana wake wachisamba. Wachiŵiri anali Yehoyakimu, wachitatu anali Zedekiya ndipo wachinai anali Salumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Yosiya: woyamba Yohanani, wachiwiri Yehoyakimu, wachitatu Zedekiya, wachinai Salumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Yosiya anali awa: Yohanani mwana wake woyamba, Yehoyakimu mwana wake wachiwiri, Zedekiya mwana wake wachitatu, Salumu mwana wake wachinayi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Yosiya: woyamba Yohanana, waciwiri Yehoyakimu, wacitatu Zedekiya, wacinai Salumu.