1 Chronicles 3:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Yekoniya, wam'ndende uja, naŵa: Sealatiele,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi mwana wa Yekoniya: Asiri, Sealatiele mwana wake,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu za Yekoniya wa mʼndende zinali izi: mwana wake Silatieli,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi mwana wa Yekoniya: Asiri, Sealitiyeli mwana wace,