1 Chronicles 3:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wake wachitatu ndi Abisalomu, mai wake anali Maaka, mwana wa Talimai, mfumu ya ku Gesuri. Mwana wake wachinai ndi Adoniya, mai wake anali Hagiti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
wachitatu Abisalomu mwana wa Maaka mwana wamkazi wa Talimai mfumu ya Gesuri, wachinai Adoniya mwana wa Hagiti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
wachitatu anali Abisalomu, mwana wa Maaka mwana wa Talimai mfumu ya Gesuri; wachinayi anali Adoniya amayi ake anali Hagiti;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
wacitatu Abisalomu mwana wa Maaka mwana wamkazi wa Talimai mfumu ya Gesuri, wacinai Adoniya mwana wa Hagiti,